Sept. 29, 2019 - Hits: 42.6K file_download : 17.8K

format_align_center Song Lyrics


Intro (Jay Jay Cee)
A aah,
Introducing! New rules!
Ah Ricco (Forces)
Ah Jay Jay Cee
1,2, 1,2 ,
Raj Nation,
PipoPipo

Hook (Jay Jay Cee)
This Game,
Ndiyosewera anthu awiri basi,
Mpaka titapanga mbiri basi,
This Game,
Malamulo ake ndi a simple,
Sitikakamiza ndipo,
X2

Verse 1(Forces)
Ah,
Chikondi any type upanga wekha choose
This game sitilola kupanga chuz (excuse)
Lol, ma haters kuwapanga confuse
Wait ah, nikuphalire ma rules
Nde udziwe thupi lakolo ndineyo mwini wake
Usadzayerekeze kumupatsa winawake
Singapeze wina nkazi oposa Iwe Ta,
Ine ndikulumbila apa chekecheke twa
Iwe Gile , tiyeko tipange zonsezi
Kusokoneza onse ma X
Azingofunsa Y
Iwe ndi ine, timakondana Z,

Hook (Jay Jay Cee)

Verse2 (Forces)
Poti dzina lako mtima mwanga nnalitypa,
Eh, Nzakukonda olo pamalo pataipa,
Marriage material apapa simakaika,
Mpaka mfana wanga udzamusintheko ma diaper,
Tikhale okondana olo tilibe tchelede,
Kuchita kumatchana ngati tili pa pelete,
Kumangodalilana ngati ogulitsa ndi ogula,
Kumachipanga value, chikondi ndichodula,
Zochenjera kusanache zipanganadi nkhwali,
Tatiyetu tikule zachibwana tiyiwale,
This Game,
Simafuna kumakhumbila,
Nzomwe tili nazo pofunika kumakhutila,

Hook(Jay Jay Cee)

Verse 3 (Jay Jay Cee)

Number 1,
Ndiyopanda referee
Kanthawi kochepa kumanditengela Patali
Number 2,
Ndikumata ngati Glue
Mpaka utanena its cool
Lamulo number 4,
Sinzakusiya for your own info
Lamulo number 5,
Usamakaike ine nkamakamba za izi
Wamva Eish,
Chikondi chathuchathu malamulo athu athu Tili tokha, mudziko lathulathu
Osamvera za ena poti sangamvetse anthu
Come along, with Mr 1,2,1,2

Hook (Jay Jay Cee)
Repeat Hook.


playlist_play Unlimited the Mixtape

Featured Music

© 2020, Malawi Media Network
Aurtial inc