April 13, 2020 - Hits: 28.2K file_download : 16.5K

format_align_center Song Lyrics


 

Verse 1 (A'chanza)
OKAY!
Manyazi tinapachika pachikale kalekale
Yesu atapanga ubale ngatiNdale n'dalephera
kuphera mphongo ya moyotu wautchale womangozinva
Nginjale kuthawa uthenga ngati Njale

Uthenga ukuwunva tsono ukuthawa cha?
Ukukanika kulalika sukuonatu kwacha?
Poti thumba la Tambe timatsegulabe ndi Tambe
Zaukulu wa Yesuyo dekha pompa ndikambe

Tatenga fungulo kwa dyabu koma sife mbala
Tazungululira moto koma osatuluka Mbala
Ngati ineyotu ndingathe iweyonso sizokulaka
Ifenso kalekalero tinkangolakalaka

Timalolera kutchedwa maina ndikuma supuka
Madzi ongopempha kudyera nsima opanda soup ka
Manyazi mayazi sitimadanda ndi zam'dziko.
Timadziwa chofunikatu ndi chimaliziko

CHORUS:
( Sir Creedy)
Hold on now! Weh a intimidate for?
Christ did a preach weh a nuh imitate.
Hold on now! Weh a hesitate for?
Answer di call never deviate.

Sitimachita (manyazi)×2
Bwanji umangokhala phwii siumachita.

Verse 2.
(David Kalirani)

The righteous are as bald as a Lion sitimaopa man tiyeni!


Mtengo wa masamba
Zipatso palibe
Mfana ndi otchuka ma diciple alibe
Ma single ndi (mbwee)
Ma video (mbwee)
Every four months akutulutsa ka EP
Tikati Bible study amadwala ma BP
Kuimba amaimbira wina aliyense
Ku Praise Team ku church kwawo kulibe aliyense
Mfana ndi otchuka  aliyense amamudziwa
Koma ku tchalitchi kwawoko samamudziwa!!
Amazungulira dziko kumenya ma show
Njale anagula nfana akupanga doe
Koma sindinanveko kuti penapake
Unamulandiritsa Yesu munthu wina wake
Umakonda kumabisala behind the music
We still need to teach the bible after the music
We still need to fast and pray after the music
Umalimba mtima ukamaima pa stage
Kuphunzitsa uthenga has alot to do with age
You can be talented and still be a baby
A famous multi talented spiritual baby
Hebrews chapter 5 verse 12 - 14
Yesu anayenda nawo pa zaka zitatu
Petulo anawina miyoyo zikwi zitatu


Iwe unabhona zaka zambirimbiri
Masamba ako adakali biriwiri
Koma sungandilozere anthu awiri
Amene analandira Yesu chifukwa cha iweyo

CHORUS (Sir Creedy)
Hold on now! Weh a intimidate for?
Christ did a preach weh a nuh imitate.
Hold on now! Weh a hesitate for?
Answer di call never deviate.

Sitimachita (manyazi)×2
Bwanji umangokhala phwii siumachita.

VERSE 3 (A'chanza)
Uh!
I am feeling blue buh i aint Manchester
But imma take a move yea imma walk Chest out
Yesu kunditana i ignore I'm insane man
Ndikuzifila Leroy ndalowa mu Sane man
Mwana wa Nkhosa lero lomwe akundiitana
He needs me to be broken for him ndine Tannah
Chomwe akufuna pamaso pake ndingoyandikila
Ndikhale wachindunji nziti manyazi nda killer


playlist_play Choice Assorted EP

Featured Music

© 2020, Malawi Media Network
Aurtial inc