Dec. 3, 2020 - Hits: 4.7K file_download : 3.3K

format_align_center Song Lyrics


Moni ft HB

Hook (HB)
Kufalitsa uthenga Ngatiso tapengaaa
Kukweza Dzinalo la Namalengaaa
Chikhristuchi tatenga
Kuwaphunzitsa onse ndikuwapasatso Moni
Landila Moni ×2
Kuchoka kumpoto mpaka kum'mweraa
Landila Moni ×2
Bwera kuno chikho cha Yehova nao mweraaa

Verse 1
I been living in my four walls visibly invisible/
People looking for substance my lyrics are metaphysical/
High above your literal innermost treasure visuals/
peripheral perspective tasteless and individual/
Forget what I said hommies am back to earth eh/
Ndimafuna mpereke moni ndithandizen/
Macheza ndi hip-hop pakhonde uthenga tifalitse/
Aja anali mu mdima pano audukira malipenga/
Ndidali phee koma mzimu wanga ngwaphokoso/
Moyo wanga plan analemba kale opanda proposal/
Yeah all the saints they understand what am talkin bout/
Am so high mutu wa Rasta pansi chikolopa
Ndinasolobana nzeru oloman/
I was jumping to hell jingo janga yacholopa/
Yanga bundle inali tchimo ka ntolo pa/
nsana gigabites for biting my soul was a total lapse/
This is for my christians amene akudziwa
They used to be corpses looking alive koma atadiwa/
lero wasintha ati wasalira Kodi
Komabe Chigonjetso ndichako landira moni

Hook (HB)
Kufalitsa uthenga Ngatiso tapengaaa
Kukweza Dzinalo la Namalengaaa
Chikhristuchi tatenga
Kuwaphunzitsa onse ndikuwapasatso Moni
Landila Moni ×2
Kuchoka kumpoto mpaka kum'mweraa
Landila Moni ×2
Bwera kuno chikho cha Yehova nao mweraaa

Verse 2
Moni upite kwa Felista wakumana ndizokhoma adha
No money Running around zoti you got a home I doubt
Fighting your demons kufika polira nazo
Praying to God daily to have your gorilla muzzled
Moni kwa Lance always searching for belonging
Coz ingakhale mu church you don't seem to find a hommy
You scared to death akadziwa zachinsisi
Zomwe zimakuvuta the response is gon be siizi (Timadziwa ife!!)
Yesu Ndiwokhulupilika ungomkhulupilira ungokhulumbilira zipatso akuumbilira
Tsono nkulu pilira ukwera bulu nchipululu ufulu waukulu wopulumukira anakugulira
Moni to God's elect in Malawi
Torchbearers ofalitsa uthenga ndimachawi
You never hear about these ones on social media
They're soldiers in the jungle they're shinning sort of a meteorite
Landila moni ngati ukudziwa suzafa
Christ is the life and resurrection and death is the transfer
Moni wanu kumastandiko tadzukani
Khristu akubwera kachikena pano akudza ndiukali

Hook


playlist_play Regenerate Singles

Featured Music

© 2020, Malawi Media Network
Aurtial inc