Dec. 4, 2020 - Hits: 4.6K file_download : 3.1K

format_align_center Song Lyrics


(A'chanza feat Saxess Prod. Mystery)

HOOK (Saxess)
Ena amadabwa
Ena amaona ngati matama
Nthawi zonse ndimakhala ndi mtendere kakaka

Mtendere
Umandinyamula nyamu (Nyamu)
Sangamake Dyabu (Dyabu)
Wachepa

Shalom
Ndili ndi Jehovah Shalom
Shalom
Iye ndi Jehovah Shalom

V.1 (A'chanza)
Okay!
Yohane 20 verse 21
Ndiyimene ndadza nayo pano nkhani
Tcherani lanu khutu mundinvetu ma mani
Talking bout peace opanda makani
I serve a big God Jehovah Shalom
Mtendere wanga sulinso shallow
Olo nyengo zanga zingavute pano
Ndimadziwa Yesu ali pa mpando
Ndiye phwando nalo nkungotenga malo
Ndili ndi chidzalo chimwemwecho tsano Yesu ali pano sindukamba nthano nthawi yathano mavuto ndakanthano ntendere watha no?
Huh!
Yesu anandibala sinchimwira dala zoipazo dhala n'dasiya ku bhala kaya nduchifwamba zonse n'dazitaya Yesu adadzitchaya

Koma mtendere
Umabwera ndikati ndi pemphere
Zonse ndimafuna ndipemphe eeh
Yesu akati mwananga ndinvetsere

HOOK (Saxess)
Ena amadabwa
Ena amaona ngati matama
Nthawi zonse ndimakhala ndi mtendere kakaka

Mtendere
Umandinyamula nyamu (Nyamu)
Sangamake Dyabu (Dyabu)
Wachepa

Shalom
Ndili ndi Jehovah Shalom
Shalom
Iye ndi Jehovah Shalom

V.2 (A'chanza
Uh!
Mtendere wa Yesu ndiwamuyaya anzanga siofeda ngati pa dzikopa
Trust in the Lord & u'll be saved akufungatira ngati Maso pa dzikopa
Amadziwa chiyambi kuchoka kumathero akalemba notes iwe m'baletu uzikopa
Anthu awone zipatso zake mwa inuyo give peace osati adzikuopani
Ndimapemedza Yahweh osati Balaam
Ndili mu Church osati m'bhalamu
Amandizutsa daily iye Alarm
Sizachipongozi so close alamu
That hour ya nkhawa biii
Aroma 15:33
Ndikatero basi thima lili ziii
Mtendere ukupanikiza just chill

Koma mtendere
Umabwera ndikati ndi pemphere
Zonse ndimafunadi ndipemphe eeh
Yesu akati mwananga ndinvetsere

HOOK (Saxess)
Ena amadabwa
Ena amaona ngati matama
Nthawi zonse ndimakhala ndi mtendere kakaka

Mtendere
Umandinyamula nyamu (Nyamu)
Sangamake Dyabu (Dyabu)
Wachepa

Shalom
Ndili ndi Jehovah Shalom
Shalom
Iye ndi Jehovah Shalom


playlist_play A'Chanza Singles

Featured Music

© 2020, Malawi Media Network
Aurtial inc